Explore
Styles
Features
Pricing
Sign in
Sign up
Sign up
Explore
Zochitika Zosowa mu Mtima
Remix
0
Share
Prompt
Anatsegula ma chats awo akale 💬 👉 “Did you eat?” 👉 “Take care please ❤️” 👉 “I’m proud of you.” Kelvin anayamba kulira 😢 👉 “No one cares like this anymore…” Nthawi yomweyo… anakumbukira tsiku limene Lina anamugwira ali ndi msungwana wina. Nkhope ya Lina… yosweka, yopweteka, koma yosalankhula kwambiri.👉 “I broke her…”Meanwhile… Lina ankayesera kupitiriza moyo wake. Anayamba: Kupita ku ntchito bwino Kukhala ndi anzake Ndipo kuyesa kuseka Koma nthawi zina… ankangokhala yekha, ndipo memories zimamubwerera zonse.
Style
Photographic
art, news, personal or emotional
Characters
Nia
Isaiah